Chikondwelero chopambana pa dziko lonse!
Kukondwelera Khilisimasi ndi chinthu cha mtengo wapatali komanso cha ulemelero chomwe chimabweletsa chimwemwe pa moyo .Pali zikondwelero zosiyanasiyana mmoyo uno koma Chikondwelero cha Khilisimasi chimaposa zonse.Chikondwelero cha Khilisimasi chimakhala ndi ulemelero wapadeladela ndi madalitso osafotokozeka.
Ndine mmodzi wa inu mu utsogoleri otumikira mu ufumu wa Mulungu, Grace Kacheto Saizi.Kwa ine ndichamwai kukutumikilani kukutumikilani pomasulira mauthenga awa ochokera kwa Jon Byler mu Chichewa.Anandipempha kuti ndikupatseni moni wa Khilisimasi!
Ambuye akudalitseni.
Ndikufunilani Khilisimasi Yabwino ndi chaka chatsopano chopambana.
|